Salimo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulemekezeni* mwanayo+ kuopera kuti Mulungu angakwiye,Ndipo mungawonongedwe nʼkuchotsedwa panjira yachilungamo,+Chifukwa mkwiyo wake umayaka mofulumira. Osangalala ndi anthu onse amene amathawira kwa iye. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:12 Nsanja ya Olonda,5/15/2006, ptsa. 17-187/15/2004, ptsa. 19-208/15/1986, tsa. 20
12 Mulemekezeni* mwanayo+ kuopera kuti Mulungu angakwiye,Ndipo mungawonongedwe nʼkuchotsedwa panjira yachilungamo,+Chifukwa mkwiyo wake umayaka mofulumira. Osangalala ndi anthu onse amene amathawira kwa iye.