Salimo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyamukani, inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga! Mudzamenya adani anga onse pachibwano.Mudzaphwanya mano a anthu oipa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:7 Nsanja ya Olonda,5/15/2011, tsa. 30
7 Nyamukani, inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga! Mudzamenya adani anga onse pachibwano.Mudzaphwanya mano a anthu oipa.+