Salimo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikaitana, mundiyankhe inu Mulungu wanga wolungama.+ Mundikonzere njira yoti ndipulumukire* mʼmasautso anga. Mundikomere mtima ndipo imvani pemphero langa. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Nsanja ya Olonda,5/15/2011, tsa. 31
4 Ndikaitana, mundiyankhe inu Mulungu wanga wolungama.+ Mundikonzere njira yoti ndipulumukire* mʼmasautso anga. Mundikomere mtima ndipo imvani pemphero langa.