-
Salimo 4:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Inu ana a anthu, kodi mudzandinyoza mʼmalo mondilemekeza mpaka liti?
Kodi mudzakonda zinthu zopanda pake komanso kufufuza zinthu zoti mundinamizire mpaka liti? (Selah)
-