Salimo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palibe anthu odzikuza amene angaime pamaso panu. Mumadana ndi anthu onse amene amachita zoipa.+