Salimo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzalowa mʼnyumba yanu+ chifukwa cha chikondi chanu chachikulu komanso chokhulupirika.+Ndidzawerama nditayangʼana kumene kuli kachisi wanu wopatulika* chifukwa chokuopani.+
7 Koma ine ndidzalowa mʼnyumba yanu+ chifukwa cha chikondi chanu chachikulu komanso chokhulupirika.+Ndidzawerama nditayangʼana kumene kuli kachisi wanu wopatulika* chifukwa chokuopani.+