Salimo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova ndinu wachilungamo,* nditsogolereni chifukwa adani anga andizungulira.Ndichotsereni zopunthwitsa mʼnjira yanu.+
8 Inu Yehova ndinu wachilungamo,* nditsogolereni chifukwa adani anga andizungulira.Ndichotsereni zopunthwitsa mʼnjira yanu.+