Salimo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikomereni mtima,* inu Yehova, chifukwa ndayamba kufooka. Ndichiritseni, inu Yehova,+ chifukwa mafupa anga akunjenjemera.
2 Ndikomereni mtima,* inu Yehova, chifukwa ndayamba kufooka. Ndichiritseni, inu Yehova,+ chifukwa mafupa anga akunjenjemera.