Salimo 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova Mulungu wanga, ine ndathawira kwa inu.+ Ndipulumutseni kwa anthu onse amene akundizunza ndipo mundilanditse.+
7 Inu Yehova Mulungu wanga, ine ndathawira kwa inu.+ Ndipulumutseni kwa anthu onse amene akundizunza ndipo mundilanditse.+