-
Salimo 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mdani wanga andithamangitse nʼkundipeza,
Andigwetsere pansi nʼkundipondaponda mpaka kufa
Ndipo andisiye nditagona pafumbi mwamanyazi. (Selah)
-