Salimo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nyamukani mutakwiya, inu Yehova.Imirirani ndi kukhaulitsa adani anga amene andikwiyira.+Dzukani nʼkundithandiza, ndipo mulamule kuti chilungamo chichitike.+
6 Nyamukani mutakwiya, inu Yehova.Imirirani ndi kukhaulitsa adani anga amene andikwiyira.+Dzukani nʼkundithandiza, ndipo mulamule kuti chilungamo chichitike.+