Salimo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzapereka chigamulo kwa mitundu ya anthu.+ Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changaKomanso mogwirizana ndi kukhulupirika kwanga.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:8 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, tsa. 6
8 Yehova adzapereka chigamulo kwa mitundu ya anthu.+ Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changaKomanso mogwirizana ndi kukhulupirika kwanga.+