Salimo 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu ndi Woweruza wolungama,+Ndipo Mulungu amapereka zigamulo kwa* oipa tsiku lililonse.