Salimo 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati munthu sakulapa,+ Mulungu amanola lupanga lake,+Amakunga uta wake nʼkukonzekera kulasa.+