Salimo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye wakumba dzenje ndipo walizamitsa,Koma adzagwera mʼdzenje limene wakumba yekhalo.+