Salimo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mavuto amene akuwayambitsawo adzabwerera pamutu pake,+Zinthu zachiwawa zimene akuchita zidzagwera paliwombo pake.
16 Mavuto amene akuwayambitsawo adzabwerera pamutu pake,+Zinthu zachiwawa zimene akuchita zidzagwera paliwombo pake.