Salimo 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munamutsitsa pangʼono poyerekeza ndi angelo,*Ndipo munamuveka ulemerero ndi ulemu ngati chisoti chachifumu. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2021, ptsa. 2-3
5 Munamutsitsa pangʼono poyerekeza ndi angelo,*Ndipo munamuveka ulemerero ndi ulemu ngati chisoti chachifumu.