Salimo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzakutamandani inu Yehova ndi mtima wanga wonse.Ndidzafotokoza za ntchito zanu zonse zodabwitsa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:1 Nsanja ya Olonda,4/15/2001, ptsa. 7-8
9 Ndidzakutamandani inu Yehova ndi mtima wanga wonse.Ndidzafotokoza za ntchito zanu zonse zodabwitsa.+