Salimo 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzakondwera ndi kusangalala chifukwa cha inu,Ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu, inu Wamʼmwambamwamba.+
2 Ndidzakondwera ndi kusangalala chifukwa cha inu,Ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu, inu Wamʼmwambamwamba.+