Salimo 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwadzudzula mitundu ya anthu+ ndipo mwawononga anthu oipa,Nʼkufufuta dzina lawo kwamuyaya.