Salimo 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu adzakumbukira anthu ovutika ndipo adzabwezera anthu amene anawapha.+Iye sadzaiwala kulira kwa anthu ovutikawo.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:12 Nsanja ya Olonda,5/15/2006, tsa. 188/15/1986, tsa. 20
12 Mulungu adzakumbukira anthu ovutika ndipo adzabwezera anthu amene anawapha.+Iye sadzaiwala kulira kwa anthu ovutikawo.+