Salimo 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Mulungu sadzaiwala anthu osauka,+Ndiponso chiyembekezo cha anthu ofatsa sichidzatha.+