Salimo 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nyamukani, inu Yehova! Musalole kuti munthu apambane. Mitundu ya anthu iweruzidwe pamaso panu.+