Salimo 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Achititseni mantha, inu Yehova,+Chititsani kuti mitundu ya anthu idziwe kuti iwo ndi anthu basi. (Selah)
20 Achititseni mantha, inu Yehova,+Chititsani kuti mitundu ya anthu idziwe kuti iwo ndi anthu basi. (Selah)