Salimo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha kudzikweza, munthu woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+
4 Chifukwa cha kudzikweza, munthu woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+