Salimo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zochita zake zikupitiriza kumuyendera bwino,+Koma zigamulo zanu sangathe kuzimvetsa.+Iye amanyogodola adani ake onse.
5 Zochita zake zikupitiriza kumuyendera bwino,+Koma zigamulo zanu sangathe kuzimvetsa.+Iye amanyogodola adani ake onse.