Salimo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nyamukani, inu Yehova.+ Inu Mulungu, chitanipo kanthu.+ Musaiwale anthu ovutika.+