-
Salimo 10:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Nʼchifukwa chiyani munthu woipa wanyoza Mulungu?
Mumtima mwake amanena kuti: “Simudzandiimba mlandu.”