-
Salimo 11:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Onani mmene anthu oipa akungira uta,
Aika mivi yawo pa chingwe cha uta,
Kuti alase anthu owongoka mtima kuchokera pamalo amdima.
-