Salimo 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu oipa akungoyendayenda popanda wowaletsa,Chifukwa chakuti ana a anthu amalimbikitsa anthu kuchita zinthu zoipa.+
8 Anthu oipa akungoyendayenda popanda wowaletsa,Chifukwa chakuti ana a anthu amalimbikitsa anthu kuchita zinthu zoipa.+