Salimo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kodi ndidzapitiriza kuvutika ndi nkhawa,Komanso tsiku lililonse ndidzakhala ndi chisoni mumtima mwanga mpaka liti? Kodi mdani wanga adzapambana mpaka liti?+
2 Kodi ndidzapitiriza kuvutika ndi nkhawa,Komanso tsiku lililonse ndidzakhala ndi chisoni mumtima mwanga mpaka liti? Kodi mdani wanga adzapambana mpaka liti?+