Salimo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chitani zimenezi kuti mdani wanga asanene kuti: “Ndamugonjetsa!” Musalole kuti adani anga asangalale chifukwa chakuti ndagwa.+
4 Chitani zimenezi kuti mdani wanga asanene kuti: “Ndamugonjetsa!” Musalole kuti adani anga asangalale chifukwa chakuti ndagwa.+