Salimo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sanena miseche ndi lilime lake,+Sachitira mnzake choipa chilichonse,+Ndipo sanyoza* anzake.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:3 Nsanja ya Olonda,10/15/1989, tsa. 129/15/1989, ptsa. 27-28