Salimo 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Sakongoza ndalama zake kuti alandire chiwongoladzanja,+Ndipo salandira chiphuphu kuti akhotetse mlandu wa munthu wosalakwa.+ Munthu aliyense amene amachita zimenezi, sadzagwedezeka.*+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:5 Nsanja ya Olonda,9/15/1989, ptsa. 29-30
5 Sakongoza ndalama zake kuti alandire chiwongoladzanja,+Ndipo salandira chiphuphu kuti akhotetse mlandu wa munthu wosalakwa.+ Munthu aliyense amene amachita zimenezi, sadzagwedezeka.*+