Salimo 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho mtima wanga ukusangalala, ndikusangalala kwambiri.* Ndipo ndikukhala motetezeka.