Salimo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nditetezeni ngati mwana wa diso lanu,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu.+