Salimo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nditetezeni kwa anthu oipa amene akundiukira,Kwa adani* ochokera kufumbi amene andizungulira.+