Salimo 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:2 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,5/1/2009, tsa. 141/15/1995, ptsa. 10-11
2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+