Salimo 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndidzaitana Yehova, amene ndi woyenera kutamandidwa,Ndipo adzandipulumutsa kwa adani anga.+