Salimo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anakwera pakerubi ndipo anabwera akuuluka.+ Mulungu anauluka mwaliwiro pamapiko a mngelo.*+