Salimo 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anaponya mivi yake nʼkuwabalalitsa.+Anaponya mphezi zake nʼkuwachititsa kuti asokonezeke.+