Salimo 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pansi pa mitsinje* panayamba kuonekera.+Maziko a dziko lapansi anayamba kuonekera chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Yehova,Komanso chifukwa cha mphamvu ya mpweya wotuluka mʼmphuno mwanu.+
15 Pansi pa mitsinje* panayamba kuonekera.+Maziko a dziko lapansi anayamba kuonekera chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Yehova,Komanso chifukwa cha mphamvu ya mpweya wotuluka mʼmphuno mwanu.+