Salimo 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kodi pali Mulungu winanso woposa Yehova?+ Nanga pali thanthwe linanso kupatula Mulungu wathu?+