Salimo 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iye amachititsa mapazi anga kuti akhale ngati a mbawala,Amachititsa kuti ndiime pamalo okwera.+