Salimo 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye amaphunzitsa manja anga kumenya nkhondo,Manja anga angathe kukunga uta wakopa.*