Salimo 18:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Inu mudzandipulumutsa kwa anthu a mtundu wanga ondipezera zifukwa.+ Mudzandiika kuti ndikhale mtsogoleri wa mitundu ya anthu.+ Anthu amene sindikuwadziwa adzanditumikira.+
43 Inu mudzandipulumutsa kwa anthu a mtundu wanga ondipezera zifukwa.+ Mudzandiika kuti ndikhale mtsogoleri wa mitundu ya anthu.+ Anthu amene sindikuwadziwa adzanditumikira.+