Salimo 18:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Anthu ochokera mʼdziko lina adzachita mantha,*Iwo adzatuluka mʼmalo awo otetezeka akunjenjemera.