Salimo 18:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mulungu woona amabwezera adani anga.+Iye amachititsa kuti mitundu ya anthu izindigonjera.