-
Salimo 19:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Dzuwalo limaoneka ngati mkwati amene akutuluka mʼchipinda chake,
Limasangalala ngati mwamuna wamphamvu amene akuthamanga pampikisano.
-