Salimo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuopa Yehova+ nʼkoyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya. Zigamulo za Yehova nʼzolondola, ndipo pa mbali iliyonse ndi zolungama.+
9 Kuopa Yehova+ nʼkoyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya. Zigamulo za Yehova nʼzolondola, ndipo pa mbali iliyonse ndi zolungama.+